IsraeliWamkulu
NdipoYehovaanatikwaAbramu, Turukaiwem’dzikolako,ndikwaabale ako,ndikunyumbayaatatewako, kunkakudzikolimenendidzakusonyeza iwe;ndipoudzakhalamdalitso:Ndipo ndidzadalitsaiwoakudalitsaiwe,ndi kutembereraiyeameneakutemberera iwe:ndipomwaiwemabanjaonsea dzikolapansiadzadalitsidwa. Genesis12:1-3

WodalamtunduumeneMulunguwawondi Yehova;ndianthuameneanawasankha akhalecholowachake.Salmo33:12

TsikulomweloYehovaanapanganapanganondiAbramu,kuti,Ndidzapatsambeu zakodzikoili,kuyambirakumtsinjewaAiguptokufikirakumtsinjewaukulu,mtsinje waFirate:Akeni,ndiAkenizi,ndiAkadimoni,ndiAhiti,ndiAperizi,ndiArefai,ndi Aamori,ndiAgirigasi,ndiAgirigasi.Genesis15:18-21
Ndipondidzakupatsaiwendimbeuzakozapambuyopako,dzikolimeneukhala mlendo,dzikolonselaKanani,likhalelakolakokosatha;ndipondidzakhalaMulungu wawo.Genesis17:8
NdipoMulunguananenandiMose,natikwaiye,InendineYehova:ndipo ndinaonekerakwaAbrahamu,kwaIsake,ndikwaYakobo,dzinalaMulungu Wamphamvuyonse,komadzinalangalaYehovasindinadziwikekwaiwo.Ndipo ndakhazikitsapanganolangandiiwo,kuwapatsadzikolaKanani,dzikolaulendo wawo,m'meneanakhalamoalendo.Eksodo6:2-4
InendineYehovaMulunguwanu,amenendinakutulutsanim’dzikolaAigupto,kuti ndikupatsenidzikolaKanani,ndikutindikhaleMulunguwanu.Levitiko25:38

Tembenukani,muyendeulendowanu,nimukekuphirilaAamori,ndikumaloonse oyandikirako,m’chigwa,ndim’mapiri,ndim’zigwa,ndim’mwela,ndim’mbalimwa nyanja,kudzikolaAkanani,ndikuLebanoni,mpakamtsinjewaukulu,mtsinjewa Firate.Taonani,ndaikadzikolopamasopanu:lowani,landiranidzikolimeneYehova analumbiriramakoloanu,Abrahamu,Isake,ndiYakobo,kutiadzawapatsaiwondi mbeuzawozapambuyopao.Deuteronomo1:7-8
“Pakutimukasungamosamalamalamuloawaonsendikuuzani,kuwachita,kukonda YehovaMulunguwanu,kuyendam’njirazakezonse,ndikum’mamatira;Pamenepo Yehovaadzaingitsaamitunduawaonsepamasopanu,ndipomudzalandiraamitundu akulundiamphamvukuposainu.Maloonseamenemapazianuadzapondapo adzakhalaanu:kuyambirachipululu,ndiLebano,kuyambirakumtsinje,mtsinjewa Firate,kufikirakunyanjayamalekezero,ndiwomalireanu.Palibemunthuadzatha kuimapamasopanu,pakutiYehovaMulunguwanuadzaikamanthaanundikuopsa kwanupadzikolonselimenemudzapondapo,mongaananenakwainu.
Deuteronomo11:22-25

Kweranim’phiriililaAbarimu,kuphirilaNebo,m’dzikolaMoabu,popenyanandi Yeriko;ndipotaonanidzikolaKanani,limenendiperekakwaanaaIsrayelilikhale lawolawo:Deuteronomo32:49
Ndipokunali,atamwaliraMosemtumikiwaYehova,YehovaananenandiYoswa mwanawaNuni,mtumikiwaMose,kuti,Mosemtumikiwangawafa;tsopano nyamuka,nuwolokeYordanouyu,iwendianthuawaonse,kulowam’dzikolimene ndiwapatsaanaaIsrayeli.Maloonseamenemapazianuadzapondapondakupatsani inu,mongandinanenandiMose.KuchokerakuchipululundiLebanoniuyu,kufikira kumtsinjewaukulu,mtsinjewaFirate,dzikolonselaAhiti,ndikufikirakuNyanja Yaikuru,kuloŵakwadzuwa,ndiwomalireanu.Sipadzakhalamunthualiyense adzaimapamasopakomasikuonseamoyowako;mongandinakhalandiMose, momwemondidzakhalandiiwe;sindidzakusiya,sindidzakutaya.Khalawamphamvu, nulimbikemtima,pakutiudzagawiraanthuawadzikolo,limenendinalumbirira makoloaokuwapatsa,likhalecolowacao.Yoswa1:1-6

NdipoawandimaikoameneanaaIsrayelianalandiram’dzikolaKanani, ameneEleazarawansembe,ndiYoswamwanawaNuni,ndiakuruamakoloa mafukoaanaaIsrayelianawagawiraakhalecholowachawo.YOSWA14:1
DavideanakanthansoHadadezeri,mwanawaRehobu,mfumuyaZoba, pakumukaiyekulanditsamalireacekumtsinjewaFirate.2SAMUELE8:3
panganolimeneanapanganandiAbrahamu,ndilumbirolakekwaIsake;Ndipo watsimikiziraichokwaYakobochikhalelamulo,ndikwaIsraelechikhale panganolosatha,Ndikuti,KwaiwendidzakupatsadzikolaKanani,likhalegawo lacholowachako;Pamenemudaliowerengeka,owerengeka,ndialendo mmenemo.1Mbiri16:16-19
NdipoDavideanakanthaHadadezerimfumuyaZobampakakuHamati, pomukaiyekukakhazikitsaufumuwakepamtsinjewaFirate.1Mbiri18:3

PanganolimeneanapanganandiAbrahamu,ndilumbirolacekwaIsake;Ndipo anatsimikiziraichokwaYakobochikhalechilamulo,ndikwaIsraelepanganolachikhalire: Ndikuti,KwaiwendidzakupatsadzikolaKanani,gawolacholowachako:Pameneiwo analiamunaowerengekamwachiwerengero;inde,owerengeka,ndialendom'menemo.
Salmo105:9-12
Ameneanakanthaamitunduakulu,naphamafumuamphamvu;Sihonimfumuya Aamori,ndiOgimfumuyaBasana,ndimaufumuonseaKanani;Dzinalanu,Yehova, lidzakhalapokosatha;ndichikumbutsochanu,Yehova,kumibadwomibadwo.
Salmo135:10-13
Ndipopanalim’chakachakhumindichisanuchakukhalaAbramum’dzikolaKanani, ndichochakachamakumiasanundiaŵirichamoyowaAbramu,ndipoYehova anaonekerakwaAbramum’chakachimenecho,natikwaiye,InendineYehovaamene ndinakuturutsam’UriKasidimu,kukupatsadzikoililikhalecholowachako.Cifukwacace tsonoyendapamasopanga,mukhaleangwiro,ndikusungamalamuloanga;pakuti ndidzakupatsaiwendimbeuzakodzikoililikhalecolowacao,kuyambirakumtsinjewa MiziraimukufikirakumtsinjewaukuluwaFirate.Yasheri13:17-18

NdipoEsauananyamukanabwererakwaYakobo,nachitazonseanalangizaNebayoti mwanawaIsmayeli;ndipoEsauanatengachumachonseanasiyaIsake,miyoyo,ndi zoweta,ng'ombe,ndichuma,ndichumachonse;sanampatsakanthuYakobombale wace;ndipoYakoboanatengadzikolonselaKanani,kuyambirakumtsinjewa
AiguptokufikirakumtsinjewaFirate,nalitengalikhalelaolacelacikhalire,ndilaana ace,ndilambeuyacepambuyopacekosatha.NdipoawandimauameneYakobo adalembam’bukulo,kuti,DzikolaKanani,ndimidziyonseyaAhiti,ndiAhivi,ndi
Ayebusi,ndiAamori,ndiAperizi,ndiAgergasi,mitunduyonseisanundiiwiri, kuyambirakumtsinjewaAigupto,kufikirakumtsinjewaFirate.Yasheri47:24,27
MoseatamwaliraYehovaanauzaYoswamwanawaNunikuti:“Nyamukani,muoloke mtsinjewaYorodano,kulowam’dzikolimenendaperekakwaanaaIsiraeli,ndipo mugawiredzikoloanaaIsiraeli.Maloonseamenemapazianuadzapondapo adzakhalaanu,kuyambirachipululuchaLebanokufikirakumtsinjewaukulu,mtsinje waPerati,ndiwomalireanu.Yasheri88:1-3

Ndipoanatikwaiye,InendineYehovaamenendinakuturutsam'Uriwa kwaAkasidi,kutindikupatsedzikolaAkananilikhalelakolakokosatha; ndipondidzakhalaMulunguwakondiwambeuzakozapambuyopako.
NdipotsikulomweloYehovaanapanganapanganondiAbramu,nati, Ndidzapatsambeuzakodzikoili,kuyambirakumtsinjewaAigupto kufikirakumtsinjewaukulu,mtsinjewaFirate,ndiAkeni,ndiAkenizi,ndi Akadimoni,ndiAperizi,ndiArefai,ndiAfarisi,ndiAhivi,ndiAamori,ndi Agirigasi,ndiAyebusi.Jubilee14:7,18
Ndipondidzakupatsaiwendimbeuzakozapambuyopakodzikolimene wakhalamlendo,dzikolaKanani,kutiulilandirelikhalelakolakokosatha, ndipoInendidzakhalaMulunguwao.Jubilee15:10

NdipondinatikwaatatewangaYakobo,MwaiweYehova adzaonongaAkanani,nadzapatsadzikolaokwaiwendikwa mbeuzakozapambuyopako.ChipanganochaLevi3:10
NdipozitathaiziadzakutulukiraniAmbuyemwini(YesuKhristu) kuunikakwachilungamo,ndipomudzabwererakudzikolanu.
Zebuloni2:32
Ndipomutathakuchepa,muchepa,mubwererandi kuvomerezaYehovaMulunguwanu;ndipoadzakubwezerani m’dzikolanumongamwachifundochakechochuluka.
ChipanganochaNafitali1:30