EpistolaWoyamba waYohane
MUTU1
1Chimenechidalikuyambirapachiyambi,chimene tidachimva,chimenetidachiwonandimasoathu,chimene tidachipenyerera,ndipomanjaathuadachigwira,cha Mawuamoyo;
2(Pakutimoyounaonekera,ndipotinauona,ndipotichita umboni,ndipotikulalikiranimoyowosathaumeneunali ndiAtate,ndipounaonekerakwaife;)
3Chimenetinachiwonandikumva,tikulalikiranikwainu, kutiinunsomukhalenachochiyanjanondiife:ndipo ndithudichiyanjanochathuchirindiAtate,ndiMwana wakeYesuKhristu
4Ndipoizitikulemberani,kutichimwemwechanu chisefukire.
5NdipouwundiuthengatidaumvakwaIye,ndipo tiulalikirakwainu,kutiMulungundiyekuunika,ndipo mwaIyemulibemdimakonse
6TikanenakutitiyanjanandiIye,ndipotikuyenda mumdima,tinama,ndipositicitacoonadi;
7Komangatitiyendam’kuunika,mongaIyealim’kuunika, tiyanjanawinandimnzake,ndipomwaziwaYesuMwana wakeutisambitsakutichotserauchimowonse.
8Tikanenakutitilibeuchimo,tidzinyengatokha,ndipo mwaifemulibechoonadi
9Ngatitivomerezamachimoathu,aliwokhulupirikandi wolungamaIye,kutiatikhululukiremachimoathu,ndi kutisambitsakutichotserachosalungamachilichonse
10Tikanenakutisitinacimwa,tiyesaIyewonama,ndipo mwaifemulibemauake
MUTU2
1Tianatanga,izindakulemberani,kutimusachimwe Ndipoakachimwawina,nkhoswetirinayekwaAtate, ndiyeYesuKristuwolungama;
2Iyendiyechiwombolochamachimoathu,osatiathuokha, komansoadzikolonselapansi.
3UmotizindikirakutitamzindikiraIye,ngatitisunga malamuloake
4Iyewakunenakuti,Ndikumudziwa,komasasunga malamuloake,ndiwabodza,ndipomwaiyemulibe choonadi
5Komaiyeameneasungamawuake,mwaiyendithu chikondichaMulunguchikhalachangwiro;
6Iyeameneanenakutiakhalamwaiyeayeneranso kuyendamongammeneiyeanayendera.
7Abale,sindikulemberanilamulolatsopano,komalamulo lakalelimenemunalinalokuyambirapachiyambiLamulo lakalendilomauamenemudawamvakuyambira pachiyambi
8Ndiponso,ndikulemberanilamulolatsopano,limenelili loonamwaiyendimwainu;
9Iyewakunenakutialim’kuunika,nadanandimbalewake, alimumdimakufikiratsopanolino.
10Iyeameneakondambalewakeakhalam’kuunika,ndipo mwaiyemulibechokhumudwitsa
11Komaiyeameneadanandimbalewakealimumdima, nayendamumdima,ndiposadziwakumeneamukako, chifukwamdimawamchititsakhungumasoake
12Ndikulemberani,tiana,chifukwamachimoanu akhululukidwachifukwachadzinalake
13Ndikulemberani,atate,chifukwamwadziwaIyeamene alikuyambirapachiyambi.Ndikulemberani,anyamata, chifukwamunagonjetsawoipayoNdikulemberani,tiana, chifukwamwadziwaAtate
14Ndakulemberani,atate,chifukwamwadziwaIyeamene alikuyambirapachiyambiNdalembakwainu,anyamata, chifukwamuliamphamvu,ndimawuaMulunguakhala mwainu,ndipomunagonjetsawoipayo.
15Musakondedzikolapansi,kapenazam’dzikolapansi Ngatiwinaakondadzikolapansi,chikondichaAtatesichili mwaiye.
16Pakutizonsezam’dzikolapansi,chilakolakochathupi, chilakolakochamaso,matamandidweamoyo,sizichokera kwaAtate,komakudzikolapansi.
17Ndipodzikolapansilipita,ndichilakolakochake; 18Tiana,inondinthawiyotsiriza:ndipomongamudamva kutiwokanaKhristuadzafika,ngakhaletsopanoalipo okanaKhristuambiri;m’menemotidziwakutindinthawi yotsiriza
19Adatulukamwaife,komasanaliaife;pakuti akadakhalaaife,akadakhalabendiife;
20KomainumudadzozedwandiWoyerayo,ndipo mudziwazinthuzonse
21Sindinakulemberanichifukwasimudziwachowonadi, komachifukwamukuchidziwa,ndikutipalibebodza lomwelimachokeram'chowonadi
22WabodzandanikomaiyeameneakanakutiYesusi Khristu?IyealiwokanaKhristu,ameneakanaAtatendi Mwana.
23YensewakukanaMwana,yemweyoalibeAtate;(koma) iyeameneabvomerezaMwanaalindiAtatenso.
24Chifukwachakelolanikutichimenemudachimva kuyambirapachiyambichikhalemwainuNgatichimene mudachimvakuyambirapachiyambichikhalamwainu, inunsomudzakhalamwaMwana,ndimwaAtate 25NdipoilindilonjezolimeneIyeanatilonjeza,ndilo moyowosatha.
26Zinthuizindakulemberanizaiwoakusokeretsainu
27KomakudzozakumenemudalandirakwaIyekukhala mwainu,ndiposimusowakutiwinaakuphunzitseni;inu, mudzakhalamwaIye
28Ndipotsopano,tiana,khalanimwaIye;kuti pakuwonekeraIye,tikhalenakokulimbikamtima,ndi kusachitamanyazipamasopakepakudzakwake
29Ngatimudziwakutialiwolungama,dziwanikutiyense wakuchitachilungamoabadwakuchokerakwaiye.
MUTU3
1Taonani,chikondichoAtatewatipatsa,kutititchedweana aMulungu;
2Okondedwa,tsopanondifeanaaMulungu,ndipo sichinaonekechimenetidzakhalapakutitidzamuwonaIye mongaali
3Ndipoyensewakukhalanachochiyembekezoichimwa Iyeadziyeretsayekha,mongaIyealiwoyera
4Aliyensewochitatchimoamaphwanyansolamulo, chifukwauchimondikuphwanyamalamulo.
5NdipomudziwakutiIyeadawonekerakudzachotsa machimoathu;ndipomwaIyemulibeuchimo.
6Yensewakukhalamwaiyesachimwa; 7Anaaang’ono,asakunyengenimunthualiyense; 8IyeameneachitatchimoaliwochokeramwaMdyerekezi; pakutimdierekeziamachimwakuyambirapachiyambi.
ChifukwachaichiMwanawaMulunguadawonekera,kuti akawonongentchitozamdierekezi
9YensewobadwamwaMulungusachitatchimo;chifukwa mbewuyakeikhalamwaiye:ndiposakhozakuchimwa, chifukwawabadwakuchokerakwaMulungu.
10MwaichiaonekeraanaaMulungu,ndianaa Mdyerekezi:yensewosachitachilungamosaliwochokera kwaMulungu,kapenaiyewosakondambalewake.
11Pakutiuwundiuthengamudaumvakuyambira pachiyambi,kutitikondanewinandimzake
12OsatimongaKaini,ameneadaliwochokeramwa woyipayo,namuphambalewakendipoanamuphaiye cifukwaninji?Chifukwantchitozakezaiyeyekhazinali zoipa,ndizambalewakezolungama.
13Musazizwe,abaleanga,ngatidzikolidainu
14Tikudziwakutitachokakuimfakupitakumoyo, chifukwatimakondaabale.Iyewosakondambalewake akhalamuimfa
15Aliyenseameneamadanandim’balewakendiwopha munthu.
16Umotizindikirachikondi,chifukwaiyeanaperekamoyo wakechifukwachaife:ndipoifetiyenerakuperekamoyo wathuchifukwachaabale.
17Komaiyeamenealindichumachadzikolapansi,naona mbalewakealiwosowa,ndikutsekerezachifundochake kwaiye,nangachikondichaMulunguchikhalamwaiye bwanji?
18Tianaanga,tisakondendimau,kapenandililime;koma m’ntchitondim’choonadi.
19Umotizindikirakutitiriachowonadi,ndipo tidzatsimikizamitimayathupamasopake
20Pakutingatimtimawathuutitsutsa,Mulunguali wamkulukuposamtimawathu,nazindikirazonse
21Okondedwa,ngatimtimawathusutitsutsa,tirinacho kulimbikamtimakwaMulungu.
22Ndipochirichonsetipempha,tilandirakwaIye, chifukwatisungamalamuloake,ndikuchitazinthu zomkondweretsapamasopake.
23Ndipoilindilamulolake,kutitikhulupiriredzinala MwanawakeYesuKhristu,ndikukondanawinandi mnzake,mongaanatilamuliraife
24Ndipoiyewakusungamalamuloakeakhalamwaiye, ndiiyemwaiyeNdipom'menemotizindikirakutiakhala mwaife,mwaMzimuumeneanatipatsaife.
MUTU4
1Okondedwa,musakhulupiriremzimuuliwonse,koma yesanimizimungatiichokerakwaMulungu:chifukwa anenerionyengaambiriadatulukakulowam'dzikolapansi
2MwaichimuzindikiraMzimuwaMulungu:mzimu uliwonseumeneuvomerezakutiYesuKhristuanadza m’thupindiwochokerakwaMulungu
3NdipomzimuuliwonseumenesuvomerezakutiYesu Khristuanadzam’thupi,suchokerakwaMulungu:ndipo uwundimzimuwawokanaKhristu,umenemunaumva kutiukudza;ndipongakhaletsopanoulikalem’dziko lapansi.
4Tianainu,ndinuaMulungu,ndipomwawalakaiwo, chifukwaiyeamenealimwainualiwamkulukuposaiye wakukhalam’dziko.
5Iwoaliadzikolapansi,chifukwachakeamalankhulaza dzikolapansi,ndipodzikolapansilikumvaiwo
6IfendifeaMulungu:wodziwaMulunguamatimvera;iye wosachokerakwaMulungusatimveraifeM’menemo tizindikiramzimuwachowonadi,ndimzimuwa kusokeretsedwa
7Okondedwa,tikondanewinandimnzake:pakutichikondi chichokerakwaMulungu;ndipoyenseameneakonda, abadwakuchokerakwaMulungu,nazindikiraMulungu
8IyewosakondasadziwaMulungu;pakutiMulungundiye chikondi.
9UmochidawonekerachikondichaMulungukwaife,kuti MulunguanatumizaMwanawakewobadwayekhakudziko lapansi,kutitikhalendimoyomwaIye.
10Umomulichikondi,sikutiifetinakondaMulungu, komakutiIyeanatikondaife,ndipoanatumaMwanawake akhalechiombolochifukwachamachimoathu.
11Okondedwa,ngatiMulunguanatikondaifekotero, ifensotiyenerakukondanawinandimnzake
12PalibemunthuadawonapoMulungu.Ngatitikondana winandimzake,Mulunguakhalamwaife,ndichikondi chakechikhalachangwiromwaife
13M’menemotizindikirakutitikhalamwaIye,ndiIye mwaife,chifukwaanatipatsamzimuwake
14Ndipoifetawona,ndipotichitaumbonikutiAtate adatumaMwanaakhaleMpulumutsiwadzikolapansi.
15IyeameneadzabvomerezakutiYesualiMwanawa Mulungu,Mulunguakhalamwaiye,ndiiyemwaMulungu 16Ifetadziwandipotakhulupirirachikondichimene MulungualinachokwaifeMulungundiyechikondi; ndipoiyeameneakhalam’chikondiakhalamwaMulungu, ndiMulunguamakhalamwaiye.
17M’menemochikondichikhalachangwiro,kutitikhale olimbikamtimam’tsikulachiweruzo;
18Mulibemantham’chikondi;komachikondichangwiro chitayakunjamantha:chifukwamanthaalinachochizunzo Woopasakhalawangwirom'chikondi
19IfetimakondaIye,chifukwaanayambaIyekutikonda. 20Ngatimunthuanenakuti,NdikondaMulungu,nadana ndimbalewake,aliwabodza;
21NdipolamuloilitilinalolochokerakwaIye,kutiiye ameneakondaMulunguakondensombalewake
MUTU5
1YensewokhulupirirakutiYesundiyeKhristu,wabadwa kuchokerakwaMulungu;
2MwaichitizindikirakutitikondaanaaMulungu,pamene tikondaMulungu,ndikusungamalamuloake.
3PakutiichindichikondichaMulungu,kutitisunge malamuloake:ndipomalamuloakesaliolemetsa
4PakutichilichonsechobadwamwaMulunguchililaka dzikolapansi:ndipoichindichigonjetsochimenechililaka dzikolapansi,ndichochikhulupirirochathu
5Ndaniiyeameneagonjetsadzikolapansi,komaiye ameneakhulupirirakutiYesualiMwanawaMulungu?
6Uyundiyeameneadadzandimadzindimwazi,ndiye YesuKhristu;osatindimadziokha,komandimadzindi mwazi.NdipoMzimundiyewochitaumboni,chifukwa Mzimundiyechowonadi
7PakutipaliatatuameneamachitiraumboniKumwamba, Atate,Mawu,ndiMzimuWoyera:ndipoatatuawaali mmodzi
8Ndipoalipoatatuakuchitiraumbonipadzikolapansi, Mzimu,ndimadzi,ndimwazi:ndipoatatuawa avomerezanam’modzi
9Ngatitilandiraumboniwaanthu,umboniwaMulungu ndiwaukulu,pakutiuwundiumboniwaMulunguumene anachitiraumbonizaMwanawake
10IyeameneakhulupiriraMwanawaMulungualinawo umbonimwaiyeyekha;chifukwasadakhulupiriraumboni umeneMulunguadauperekawaMwanawake
11Ndipouwundiumboni,kutiMulunguanatipatsaife moyowosatha,ndipomoyoumenewuulimwaMwana wake
12IyeamenealindiMwanaalinawomoyo;ndipoiye amenealibeMwanawaMulungualibemoyo
13Zinthuizindakulemberaniinu,akukhulupiriradzinala MwanawaMulungu;kutimudziwekutimulinawomoyo wosatha,ndikutimukhulupirirepadzinalaMwanawa Mulungu
14NdipoichindichidalirochimenetilinachomwaIye, kutingatitipemphakanthumongamwachifunirochake, amatimvera;
15Ndipongatitidziwakutiamatimveram’chilichonse chimenetipempha,tidziwakutitirinazozopemphazimene tidazipemphakwaIye
16Ngatiwinaawonam’balewakeakuchimwatchimo losatilakuimfa,apemphere,ndipoiyeadzam’patsamoyo chifukwachaiwoameneamachimwaosatikuimfaPali tchimolakuimfa:sindikunenakutialipempherereilo.
17Chisalungamochonsendiuchimo:ndipopalitchimo losatilakuimfa
18TidziwakutiyensewobadwamwaMulungusachimwa; komaiyewobadwamwaMulunguadzisunga,ndipo woipayosamkhudzaiye
19NdipotidziwakutindifeaMulungu,ndipodzikolonse lapansiligonamwawoipayo
20NdipotidziwakutiMwanawaMulunguwafika, natipatsaifechidziwitso,kutitizindikireWoonayo,ndipo tirimwaWoonayo,mwaMwanawakeYesuKristuUyu ndiyeMulunguwoona,ndimoyowosatha.
21Tiana,pewanimafanoAmene